3 YOHANE Mau Oyamba
Mau Oyamba
Kalata yachitatu yolembedwa ndi mtumwi Yohane inalembedwa ndi “Mkuluyo” kulembera mtsogoleri wa mpingo dzina lake Gayo. Mlembiyo akumuyamikira Gayo chifukwa cha kuthandiza akhristu ena, komanso akuwachenjeza za munthu wina dzina lake Diotrefe.
Za mkatimu
Mau oyamba 1.1-4
Gayo akumulemekeza 1.5-8
Diotrefe akumudzudzula 9-10
Demetrio akumuyamikira 1.11-12
Mau omaliza 1.13-15
Currently Selected:
3 YOHANE Mau Oyamba: BLPB2014
Highlight
Share
Copy

Want to have your highlights saved across all your devices? Sign up or sign in
The Bible in Chichewa Published as Buku Lopatulika
Bible Society of Malawi