1
MASALIMO 85:2
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Munachotsa mphulupulu ya anthu anu, munafotsera zolakwa zao zonse.
Compare
Explore MASALIMO 85:2
2
MASALIMO 85:10
Chifundo ndi choonadi zakomanizana; chilungamo ndi mtendere zapsompsonana.
Explore MASALIMO 85:10
3
MASALIMO 85:9
Indedi chipulumutso chake chili pafupi ndi iwo akumuopa Iye; kuti m'dziko mwathu mukhale ulemu.
Explore MASALIMO 85:9
4
MASALIMO 85:13
Chilungamo chidzamtsogolera; nichidzamkonzera mapazi ake njira.
Explore MASALIMO 85:13
Home
Bible
Plans
Videos