1
MASALIMO 86:11
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Mundionetse njira yanu, Yehova; ndidzayenda m'choonadi chanu, muumbe mtima wanga ukhale umodzi kuti uliope dzina lanu.
Compare
Explore MASALIMO 86:11
2
MASALIMO 86:5
Pakuti Inu, Ambuye, ndinu wabwino, ndi wokhululukira, ndi wa chifundo chochulukira onse akuitana Inu.
Explore MASALIMO 86:5
3
MASALIMO 86:15
Koma Inu, Ambuye, ndinu Mulungu wansoni ndi wachisomo, wopatsa mtima msanga, ndi wochulukira chifundo ndi choonadi.
Explore MASALIMO 86:15
4
MASALIMO 86:12
Ndidzakuyamikani, Ambuye, Mulungu wanga, ndi mtima wanga wonse; ndipo ndidzalemekeza dzina lanu nthawi zonse.
Explore MASALIMO 86:12
5
MASALIMO 86:7
Tsiku la msauko wanga ndidzaitana Inu; popeza mudzandivomereza.
Explore MASALIMO 86:7
Home
Bible
Plans
Videos