1
MASALIMO 83:18
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Kuti adziwe kuti inu nokha, dzina lanu ndinu Yehova, ndinu Wam'mwambamwamba pa dziko lonse lapansi.
Compare
Explore MASALIMO 83:18
2
MASALIMO 83:1
Mulungu musakhale chete; musakhale duu, osanena kanthu, Mulungu.
Explore MASALIMO 83:1
3
MASALIMO 83:16
Achititseni manyazi pankhope pao; kuti afune dzina lanu, Yehova.
Explore MASALIMO 83:16
Home
Bible
Plans
Videos