1
MASALIMO 82:6
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ndinati Ine, Inu ndinu milungu, ndi ana a Wam'mwambamwamba nonsenu.
Compare
Explore MASALIMO 82:6
2
MASALIMO 82:3
Weruzani osauka ndi amasiye; weruzani molungama ozunzika ndi osowa.
Explore MASALIMO 82:3
3
MASALIMO 82:4
Pulumutsani osauka ndi aumphawi; alanditseni m'dzanja la oipa.
Explore MASALIMO 82:4
4
MASALIMO 82:8
Ukani, Mulungu, weruzani dziko lapansi; pakuti Inu mudzalandira amitundu onse.
Explore MASALIMO 82:8
Home
Bible
Plans
Videos