1
MASALIMO 81:10
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ine ndine Yehova Mulungu wako amene ndinakukweza kukuchotsa kudziko la Ejipito; yasamitsa pakamwa pako ndipo ndidzalidzaza.
Compare
Explore MASALIMO 81:10
2
MASALIMO 81:13-14
Ha! Akadandimvera anthu anga, akadayenda m'njira zanga Israele! Ndikadagonjetsa adani ao msanga, ndikadabweza dzanja langa pa owasautsa.
Explore MASALIMO 81:13-14
Home
Bible
Plans
Videos