1
YEREMIYA 14:22
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Mwa zachabe za mitundu ya anthu zilipo kodi, zimene zingathe kuvumbitsa mvula? Kodi si ndinu, Yehova, Mulungu wathu? Ndipo tidzakudikirani Inu; pakuti munalenga zonse zimenezi.
Compare
Explore YEREMIYA 14:22
2
YEREMIYA 14:7
Zingakhale zoipa zathu zititsutsa ife, chitani Inu chifukwa cha dzina lanu, Yehova; pakuti zobwerera zathu zachuluka; takuchimwirani Inu.
Explore YEREMIYA 14:7
3
YEREMIYA 14:20-21
Tivomereza, Yehova, chisalungamo chathu, ndi choipa cha makolo athu; pakuti takuchimwirani Inu. Musatinyoze ife, chifukwa cha dzina lanu; musanyazitse mpando wachifumu wa ulemerero wanu; mukumbukire musasiye pangano lanu lopangana ndi ife.
Explore YEREMIYA 14:20-21
Home
Bible
Plans
Videos