1
2 MAFUMU 6:17
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ndipo Elisa anapemphera, nati, Yehova, mumtsegulire maso ake kuti aone. Pamenepo Yehova anamtsegulira maso mnyamatayo, napenya iye, ndipo taonani, paphiripo panadzala ndi akavalo ndi magaleta amoto akumzinga Elisa.
Compare
Explore 2 MAFUMU 6:17
2
2 MAFUMU 6:16
Nati iye, Usaopa, pakuti okhala pamodzi ndi ife achuluka koposa aja okhala pamodzi ndi iwo.
Explore 2 MAFUMU 6:16
3
2 MAFUMU 6:15
Ndipo atalawirira mamawa mnyamata wa munthu wa Mulungu, natuluka, taonani, khamu la nkhondo linazinga mudzi ndi akavalo ndi magaleta. Ndi mnyamata wake ananena naye, Kalanga ine, mbuye wanga! Tichitenji?
Explore 2 MAFUMU 6:15
4
2 MAFUMU 6:18
Ndipo atatsikira pali iye, Elisa anapemphera kwa Yehova, nati, Mukanthe mtundu uwu uchite khungu. Ndipo Iye anawakantha, nawachititsa khungu, monga mwa mau a Elisa.
Explore 2 MAFUMU 6:18
5
2 MAFUMU 6:6
Nati munthu wa Mulungu, Yagwera pati? Namuonetsapo yagwera. Pamenepo anadula kamtengo, nakaponya pomwepo, nayandamitsa nkhwangwayo.
Explore 2 MAFUMU 6:6
6
2 MAFUMU 6:5
Ndipo wina analinkudula mtengo nkhwangwa inagwa m'madzi; ndipo anafuula, nati, Kalanga ine mbuyanga! Popeza njobwereka.
Explore 2 MAFUMU 6:5
7
2 MAFUMU 6:7
Nati, Katole. Natambasula dzanja lake, naitenga.
Explore 2 MAFUMU 6:7
Home
Bible
Plans
Videos