1
2 MAFUMU 5:1
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ndipo Naamani kazembe wa khamu la nkhondo la mfumu ya Aramu anali munthu womveka pamaso pa mbuyake, ndi waulemu; popeza mwa iye Yehova adapulumutsa Aaramu; ndiyenso ngwazi, koma wakhate.
Compare
Explore 2 MAFUMU 5:1
2
2 MAFUMU 5:10
Ndipo Elisa anamtumira mthenga, ndi kuti, Kasambe m'Yordani kasanu ndi kawiri, ndi mnofu wako udzabwerera momwe, nudzakhala wokonzeka.
Explore 2 MAFUMU 5:10
3
2 MAFUMU 5:14
Potero anatsika, namira m'Yordani kasanu ndi kawiri, monga adanena munthu wa Mulunguyo; ndi mnofu wake unabwera monga mnofu wa mwana wamng'ono, nakonzeka.
Explore 2 MAFUMU 5:14
4
2 MAFUMU 5:11
Koma Naamani adapsa mtima, nachoka, nati, Taona, ndinati m'mtima mwanga, kutuluka adzanditulukira, nadzaima ndi kuitana pa dzina la Yehova Mulungu wake, ndi kuweyula dzanja lake pamalopo, ndi kuchiritsa wakhateyo.
Explore 2 MAFUMU 5:11
5
2 MAFUMU 5:13
Pamenepo anyamata ake anasendera, nanena naye, nati, Atate wanga, mneneri akadakuuzani chinthu chachikulu, simukadachichita kodi? Koposa kotani nanga ponena iye, Samba, nukonzeke?
Explore 2 MAFUMU 5:13
6
2 MAFUMU 5:3
Nati uyu kwa mbuyake wamkazi, Mbuye wanga akadakhala kwa mneneri ali m'Samariya, akadamchiritsa khate lake.
Explore 2 MAFUMU 5:3
Home
Bible
Plans
Videos