1
2 MAFUMU 7:1
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ndipo Elisa anati, Mverani mau a Yehova; atero Yehova, Mawa dzuwa lino adzagula muyeso wa ufa ndi sekeli, adzagulanso miyeso iwiri ya barele ndi sekeli, pa chipata cha Samariya.
Compare
Explore 2 MAFUMU 7:1
2
2 MAFUMU 7:3
Koma polowera pa chipata panali amuna anai akhate, nanenana wina ndi mnzake, Tikhaliranji kuno mpaka kufa?
Explore 2 MAFUMU 7:3
3
2 MAFUMU 7:2
Pamenepo kazembe amene mfumu ankatsamira pa dzanja lake anamyankha munthu wa Mulungu, nati, Taonani, Yehova angachite mazenera m'mwamba chidzachitika ichi kodi? Nati iye, Taona, udzachiona ndi maso ako, koma iwe sudzadyako ai.
Explore 2 MAFUMU 7:2
Home
Bible
Plans
Videos