Ntc. 14:9-10
Ntc. 14:9-10 BLY-DC
Iyeyo ankamvetsera pamene Paulo ankalankhula. Paulo adampenyetsetsa, ndipo ataona kuti munthuyo ali ndi chikhulupiriro choti nkuchira, adanena mokweza mau kuti, “Wongola miyendo yako, imirira.” Pomwepo munthuyo adadzambatuka nkuyamba kuyenda.