YouVersion Logo
Search Icon

NAHUMU Mau Oyamba

Mau Oyamba
Bukuli ndi ndakatulo yokondwerera kupasuka kwa Ninive, mzinda waukulu wa Aasiriya amene ankazunza Aisraele kuyambira kale. Kupasuka kwa mzindawo kuwoneka ngati chilango cha Mulungu chogwera anthu onyada ndi ankhanza.
Za mkatimu
Chauta aimba Ninive mlandu 1.1-15
Kupasuka kwa mzindawo 2.1—3.19

Currently Selected:

NAHUMU Mau Oyamba: BLPB2014

Highlight

Share

Copy

None

Want to have your highlights saved across all your devices? Sign up or sign in