YouVersion Logo
Search Icon

YUDA Mau Oyamba

Mau Oyamba
Kalata yolembedwa ndi mtumwi Yuda analembedwa pofuna kuwachenjeza za aphunzitsi onyenga amene amadzitcha okhulupirira. Mkalata iyi yachidule imene nkhani zake zikufanana ndi za mu Kalata yachiwiri yolembedwa ndi mtumwi Petro, ndipo wolembayo akuwalimbikitsa awerengi ake kuti “mulimbanetu chifukwa cha chikhulupiriro chapatsidwa kamodzi kwa oyera mtima”.
Za mkatimu
Mau oyamba 1.1-2
Khalidwe labwino, chiphunzitso, ndi mathero a aphunzitsi onyenga 1.3-16
Awalimbikitsa asunge chikhulupiriro 1.17-23
Mdalitso 1.24-25

Currently Selected:

YUDA Mau Oyamba: BLPB2014

Highlight

Share

Copy

None

Want to have your highlights saved across all your devices? Sign up or sign in