1
Gen. 33:4
Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa
Koma Esau adathamanga kukakumana naye, namkumbatira, ndi kumlonjera pakumumpsompsona. Onse aŵiriwo ankangolira.
Compare
Explore Gen. 33:4
2
Gen. 33:20
Adamanga guwa pomwepo, nalitcha El-Elohe-Israele, ndiye kuti Mulungu, Mulungu wa Israele.
Explore Gen. 33:20
Home
Bible
Plans
Videos