1
MASALIMO 95:6-7
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Tiyeni, tipembedze tiwerame; tigwade pamaso pa Yehova, amene anatilenga. Pakuti Iye ndiye Mulungu wathu, ndipo ife ndife anthu a pabusa pake, ndi nkhosa za m'dzanja mwake. Lero, mukamva mau ake!
Compare
Explore MASALIMO 95:6-7
2
MASALIMO 95:1-2
Tiyeni tiimbire Yehova mokondwera; tifuule kwa thanthwe la chipulumutso chathu. Tidze nacho chiyamiko pamaso pake, timfuulire Iye mokondwera ndi nyimbo.
Explore MASALIMO 95:1-2
3
MASALIMO 95:3
Pakuti Yehova ndiye Mulungu wamkulu; ndi mfumu yaikulu yoposa milungu yonse.
Explore MASALIMO 95:3
4
MASALIMO 95:4
Malo ozama a dziko lapansi ali m'dzanja lake; chuma cha m'mapiri chomwe ndi chake.
Explore MASALIMO 95:4
Home
Bible
Plans
Videos