1
MASALIMO 94:19
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Pondichulukira zolingalira zanga m'kati mwanga, zotonthoza zanu zikondweretsa moyo wanga.
Compare
Explore MASALIMO 94:19
2
MASALIMO 94:18
Pamene ndinati, Litereka phazi langa, chifundo chanu, Yehova, chinandichirikiza.
Explore MASALIMO 94:18
3
MASALIMO 94:22
Koma Yehova wakhala msanje wanga; ndi Mulungu wanga thanthwe lothawirapo ine.
Explore MASALIMO 94:22
4
MASALIMO 94:12
Wodala munthu amene mumlanga, Yehova; ndi kumphunzitsa m'chilamulo chanu
Explore MASALIMO 94:12
5
MASALIMO 94:17
Akadapanda kukhala thandizo langa Yehova, moyo wanga ukadakhala kuli chete.
Explore MASALIMO 94:17
6
MASALIMO 94:14
Pakuti Yehova sadzasiya anthu ake, ndipo sadzataya cholandira chake.
Explore MASALIMO 94:14
Home
Bible
Plans
Videos