1
MASALIMO 90:12
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Mutidziwitse kuwerenga masiku athu motero, kuti tikhale nao mtima wanzeru.
Compare
Explore MASALIMO 90:12
2
MASALIMO 90:17
Ndipo chisomo chake cha Yehova Mulungu wathu chikhalire pa ife; ndipo mutikhazikitsire ife ntchito ya manja athu; inde, ntchito ya manja athu muikhazikitse.
Explore MASALIMO 90:17
3
MASALIMO 90:14
Mutikhutitse nacho chifundo chanu m'mawa; ndipo tidzafuula mokondwera ndi kukondwera masiku athu onse.
Explore MASALIMO 90:14
4
MASALIMO 90:2
Asanabadwe mapiri, kapena musanalenge dziko lapansi, ndi lokhalamo anthu, inde, kuyambira nthawi yosayamba kufikira nthawi yosatha, Inu ndinu Mulungu.
Explore MASALIMO 90:2
5
MASALIMO 90:1
Ambuye, Inu munatikhalira mokhalamo m'mibadwomibadwo.
Explore MASALIMO 90:1
6
MASALIMO 90:4
Pakuti pamaso panu zaka zikwi zikhala ngati dzulo, litapita, ndi monga ulonda wa usiku.
Explore MASALIMO 90:4
Home
Bible
Plans
Videos