1
MASALIMO 89:15
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Odala anthu odziwa liu la lipenga; ayenda m'kuunika kwa nkhope yanu, Yehova.
Compare
Explore MASALIMO 89:15
2
MASALIMO 89:14
Chilungamo ndi chiweruzo ndiwo maziko a mpando wachifumu wanu; chifundo ndi choonadi zitsogolera pankhope panu.
Explore MASALIMO 89:14
3
MASALIMO 89:1
Ndidzaimbira zachifundo za Yehova nthawi yonse, pakamwa panga ndidzadziwitsira chikhulupiriko chanu ku mibadwomibadwo.
Explore MASALIMO 89:1
4
MASALIMO 89:8
Yehova, Mulungu wa makamu, wamphamvu ndani wonga Inu, Yehova? Ndipo chikhulupiriko chanu chikuzingani.
Explore MASALIMO 89:8
Home
Bible
Plans
Videos