1
MATEYU 3:8
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Onetsani inu zipatso zakuyenera kutembenuka mtima
Compare
Explore MATEYU 3:8
2
MATEYU 3:17
ndipo onani, mau akuchokera kumiyamba akuti, Uyu ndiye mwana wanga wokondedwa, mwa Iyeyu ndikondwera.
Explore MATEYU 3:17
3
MATEYU 3:16
Ndipo Yesu, pamene anabatizidwa, pomwepo anatuluka m'madzi: ndipo onani, miyamba inamtsegukira Iye, ndipo anapenya Mzimu wa Mulungu wakutsika ngati nkhunda nudza nutera pa Iye
Explore MATEYU 3:16
4
MATEYU 3:11
Inetu ndikubatizani inu ndi madzi kuloza ku kutembenuka mtima; koma Iye wakudza pambuyo panga, ali wakundiposa mphamvu, amene sindiyenera kunyamula nsapato zake: Iyeyu adzakubatizani inu ndi Mzimu Woyera ndi moto
Explore MATEYU 3:11
5
MATEYU 3:10
Ndiponso tsopano lino nkhwangwa yaikidwa pa mizu ya mitengo: chifukwa chake mtengo uliwonse wosabala zipatso zabwino udulidwa nuponyedwa pamoto.
Explore MATEYU 3:10
6
MATEYU 3:3
Pakuti uyu ndiye ananenayo Yesaya mneneri, kuti, Mau a wofuula m'chipululu, konzani khwalala la Ambuye, lungamitsani njira zake.
Explore MATEYU 3:3
Home
Bible
Plans
Videos