1
MATEYU 4:4
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Koma Iye anayankha nati, Kwalembedwa, Munthu sadzakhala ndi moyo ndi mkate wokha, koma ndi mau onse akutuluka m'kamwa mwa Mulungu.
Compare
Explore MATEYU 4:4
2
MATEYU 4:10
Pomwepo Yesu ananena kwa iye, Choka Satana, pakuti kwalembedwa, Ambuye Mulungu wako udzamgwadira, ndipo Iye yekhayekha udzamlambira.
Explore MATEYU 4:10
3
MATEYU 4:7
Yesu ananena naye, Ndiponso kwalembedwa, Usamuyese Ambuye Mulungu wako.
Explore MATEYU 4:7
4
MATEYU 4:1-2
Pamenepo Yesu anatengedwa ndi Mzimu kunka kuchipululu kukayesedwa ndi mdierekezi. Ndipo pamene Iye analibe kudya masiku makumi anai usana ndi usiku, pambuyo pake anamva njala.
Explore MATEYU 4:1-2
5
MATEYU 4:19-20
Ndipo Iye ananena nao, Tiyeni pambuyo panga, ndidzakusandutsani asodzi a anthu. Ndipo iwo anasiya pomwepo makokawo, namtsata Iye.
Explore MATEYU 4:19-20
6
MATEYU 4:17
Kuyambira pamenepo Yesu anayamba kulalikira, ndi kunena, Tembenukani mitima, pakuti Ufumu wa Kumwamba wayandikira.
Explore MATEYU 4:17
Home
Bible
Plans
Videos