1
YAKOBO 3:17
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Koma nzeru yochokera kumwamba iyamba kukhala yoyera, nikhalanso yamtendere, yaulere, yomvera bwino, yodzala chifundo ndi zipatso zabwino, yopanda tsankho, yosadzikometsera pamaso.
Compare
Explore YAKOBO 3:17
2
YAKOBO 3:13
Ndani ali wanzeru, ndi waluso mwa inu? Aonetsere ndi mayendedwe ake abwino ntchito zake mu nzeru yofatsa.
Explore YAKOBO 3:13
3
YAKOBO 3:18
Ndipo chipatso cha chilungamo chifesedwa mumtendere kwa iwo akuchita mtendere.
Explore YAKOBO 3:18
4
YAKOBO 3:16
Pakuti pomwe pali kaduka ndi zotetana, pamenepo pali chisokonekero ndi chochita choipa chilichonse.
Explore YAKOBO 3:16
5
YAKOBO 3:9-10
Timayamika Ambuye ndi Atate nalo; nalonso timatemberera anthu, okhala monga mwa mafanizidwe a Mulungu; Mochokera m'kamwa momwemo mutuluka chiyamiko ndi temberero. Abale anga, izi siziyenera kutero.
Explore YAKOBO 3:9-10
6
YAKOBO 3:6
Ndipo lilime ndilo moto; ngati dziko la chosalungama mwa ziwalo zathu laikika lilime, ndili lodetsa thupi lonse, niliyatsa mayendedwe a chibadwidwe, ndipo liyatsidwa ndi Gehena.
Explore YAKOBO 3:6
7
YAKOBO 3:8
koma lilime palibe munthu akhoza kulizoloweretsa; lili choipa chotakataka, lodzala ndi ululu wakupha.
Explore YAKOBO 3:8
8
YAKOBO 3:1
Musakhale aphunzitsi ambiri, abale anga, podziwa kuti tidzalangika koposa.
Explore YAKOBO 3:1
Home
Bible
Plans
Videos