1
DEUTERONOMO 32:4
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Thanthwe, ntchito yake ndi yangwiro; pakuti njira zake zonse ndi chiweruzo; Mulungu wokhulupirika ndi wopanda chisalungamo; Iye ndiye wolungama ndi wolunjika.
Compare
Explore DEUTERONOMO 32:4
2
DEUTERONOMO 32:39
Tapenyani tsopano kuti Ine ndine Iye, ndipo palibe mulungu koma Ine; ndipha Ine, ndikhalitsanso ndi moyo, ndikantha, ndichizanso Ine; ndipo palibe wakulanditsa m'dzanja langa.
Explore DEUTERONOMO 32:39
3
DEUTERONOMO 32:3
Pakuti ndidzalalika dzina la Yehova. Nenani kuti Mulungu wathu ndi wamkulu.
Explore DEUTERONOMO 32:3
Home
Bible
Plans
Videos