1
DEUTERONOMO 31:6
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Khalani amphamvu, limbikani mitima, musamachita mantha, kapena kuopsedwa chifukwa cha iwowa; popeza Yehova Mulungu wanu ndiye amene amuka nanu; Iye sadzakusowani, kapena kukusiyani.
Compare
Explore DEUTERONOMO 31:6
2
DEUTERONOMO 31:8
Ndipo Yehova, Iye ndiye amene akutsogolera; Iye adzakhala ndi iwe, Iye sadzakusowa kapena kukusiya; usamachita mantha, usamatenga nkhawa.
Explore DEUTERONOMO 31:8
3
DEUTERONOMO 31:7
Ndipo Mose anaitana Yoswa, nati naye pamaso pa Israele wonse, Khala wamphamvu, nulimbe mtima; pakuti udzalowa nao anthu awa m'dziko limene Yehova analumbirira makolo ao kuwapatsa ilo; ndipo iwe udzawalandiritsa ilo.
Explore DEUTERONOMO 31:7
Home
Bible
Plans
Videos