1
AMOSI 5:24
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Koma chiweruzo chiyende ngati madzi, ndi chilungamo ngati mtsinje wosefuka.
Compare
Explore AMOSI 5:24
2
AMOSI 5:14
Funani chokoma, si choipa ai; kuti mukhale ndi moyo; motero Yehova Mulungu wa makamu adzakhala ndi inu, monga munena.
Explore AMOSI 5:14
3
AMOSI 5:15
Danani nacho choipa, nimukonde chokoma; nimukhazikitse chiweruzo kuchipata; kapena Yehova Mulungu wa makamu adzachitira chifundo otsala a Yosefe.
Explore AMOSI 5:15
4
AMOSI 5:4
Pakuti atero Yehova kwa nyumba ya Israele, Mundifunefune Ine, ndipo mudzakhala ndi moyo
Explore AMOSI 5:4
Home
Bible
Plans
Videos