1
MACHITIDWE A ATUMWI 6:3-4
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Chifukwa chake, abale, yang'anani mwa inu amuna asanu ndi awiri a mbiri yabwino, odzala ndi Mzimu ndi nzeru, amene tikawaike asunge ntchito iyi. Koma ife tidzalimbika m'kupemphera, ndi kutumikira mau.
Compare
Explore MACHITIDWE A ATUMWI 6:3-4
2
MACHITIDWE A ATUMWI 6:7
Ndipo mau a Mulungu anakula; ndipo chiwerengero cha ophunzira chidachulukatu ku Yerusalemu; ndipo khamu lalikulu la ansembe linamvera chikhulupirirocho.
Explore MACHITIDWE A ATUMWI 6:7
Home
Bible
Plans
Videos