1
MACHITIDWE A ATUMWI 19:6
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ndipo pamene Paulo anaika manja ake pa iwo, Mzimu Woyera anadza pa iwo; ndipo analankhula ndi malilime, nanenera.
Compare
Explore MACHITIDWE A ATUMWI 19:6
2
MACHITIDWE A ATUMWI 19:11-12
Ndipo Mulungu anachita zamphamvu za pa zokha ndi manja a Paulo; kotero kuti anamuka nazo kwa odwala nsalu zopukutira ndi za pantchito, zochokera pathupi pake, ndipo nthenda zinawachokera, ndi ziwanda zinatuluka.
Explore MACHITIDWE A ATUMWI 19:11-12
3
MACHITIDWE A ATUMWI 19:15
Ndipo unayankha mzimu woipa, nuti kwa iwo, Yesu ndimzindikira, ndi Paulo ndimdziwa, koma inu ndinu ayani?
Explore MACHITIDWE A ATUMWI 19:15
Home
Bible
Plans
Videos