MACHITIDWE A ATUMWI 19:11-12
MACHITIDWE A ATUMWI 19:11-12 BLPB2014
Ndipo Mulungu anachita zamphamvu za pa zokha ndi manja a Paulo; kotero kuti anamuka nazo kwa odwala nsalu zopukutira ndi za pantchito, zochokera pathupi pake, ndipo nthenda zinawachokera, ndi ziwanda zinatuluka.