1
MACHITIDWE A ATUMWI 17:27
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
kuti afunefune Mulungu, kapena akamfufuze ndi kumpeza, ngakhale sakhala patali ndi yense wa ife
Compare
Explore MACHITIDWE A ATUMWI 17:27
2
MACHITIDWE A ATUMWI 17:26
ndipo ndi mmodzi analenga mitundu yonse ya anthu, kuti akhale ponse pa nkhope ya dziko lapansi, atapangiratu nyengo zao, ndi malekezero a pokhala pao
Explore MACHITIDWE A ATUMWI 17:26
3
MACHITIDWE A ATUMWI 17:24
Mulungu amene analenga dziko lapansi ndi zonse zili momwemo, Iyeyo, ndiye mwini kumwamba ndi dziko lapansi, sakhala m'nyumba za kachisi zomangidwa ndi manja
Explore MACHITIDWE A ATUMWI 17:24
4
MACHITIDWE A ATUMWI 17:31
chifukwa anapangira tsiku limene adzaweruza dziko lokhalamo anthu m'chilungamo, ndi munthu amene anamuikiratu; napatsa anthu onse chitsimikizo, pamene anamuukitsa Iye kwa akufa.
Explore MACHITIDWE A ATUMWI 17:31
5
MACHITIDWE A ATUMWI 17:29
Popeza tsono tili mbadwa za Mulungu, sitiyenera kulingalira kuti umulungu uli wofanafana ndi golide, kapena siliva, kapena mwala, wolocha ndi luso ndi zolingalira za anthu.
Explore MACHITIDWE A ATUMWI 17:29
Home
Bible
Plans
Videos