MACHITIDWE A ATUMWI 17:29
MACHITIDWE A ATUMWI 17:29 BLPB2014
Popeza tsono tili mbadwa za Mulungu, sitiyenera kulingalira kuti umulungu uli wofanafana ndi golide, kapena siliva, kapena mwala, wolocha ndi luso ndi zolingalira za anthu.