1
MACHITIDWE A ATUMWI 15:11
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Koma tikhulupirira tidzapulumuka mwa chisomo cha Ambuye Yesu Khristu, monga iwo omwe.
Compare
Explore MACHITIDWE A ATUMWI 15:11
2
MACHITIDWE A ATUMWI 15:8-9
Ndipo Mulungu, amene adziwa mtima, anawachitira umboni; nawapatsa Mzimu Woyera, monga anatipatsa ife; ndipo sanalekanitsa ife ndi iwo, nayeretsa mitima yao m'chikhulupiriro.
Explore MACHITIDWE A ATUMWI 15:8-9
Home
Bible
Plans
Videos