1
MACHITIDWE A ATUMWI 13:2-3
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ndipo pa kutumikira Ambuye iwowa, ndi kusala chakudya, Mzimu Woyera anati, Mundipatulire Ine Barnabasi ndi Saulo ku ntchito imene ndinawaitanirako. Pamenepo, m'mene adasala chakudya ndi kupemphera ndi kuika manja pa iwo, anawatumiza amuke.
Compare
Explore MACHITIDWE A ATUMWI 13:2-3
2
MACHITIDWE A ATUMWI 13:39
ndipo mwa Iye yense wokhulupirira ayesedwa wolungama kumchotsera zonse zimene simunangathe kudzichotsera poyesedwa wolungama ndi chilamulo cha Mose.
Explore MACHITIDWE A ATUMWI 13:39
3
MACHITIDWE A ATUMWI 13:47
Pakuti kotero anatilamula Ambuye ndi kuti, Ndakuika iwe kuunika kwa amitundu, kuti udzakhala iwe chipulumutso kufikira malekezero a dziko.
Explore MACHITIDWE A ATUMWI 13:47
Home
Bible
Plans
Videos