YouVersion Logo
Search Icon

MACHITIDWE A ATUMWI 13:2-3

MACHITIDWE A ATUMWI 13:2-3 BLPB2014

Ndipo pa kutumikira Ambuye iwowa, ndi kusala chakudya, Mzimu Woyera anati, Mundipatulire Ine Barnabasi ndi Saulo ku ntchito imene ndinawaitanirako. Pamenepo, m'mene adasala chakudya ndi kupemphera ndi kuika manja pa iwo, anawatumiza amuke.