1
1 PETRO 4:8
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
koposa zonse mukhale nacho chikondano chenicheni mwa inu nokha; pakuti chikondano chikwiriritsa unyinji wa machimo
Compare
Explore 1 PETRO 4:8
2
1 PETRO 4:10
monga yense walandira mphatso, mutumikirane nayo, ngati adindo okoma a chisomo cha mitundumitundu cha Mulungu
Explore 1 PETRO 4:10
3
1 PETRO 4:11
akalankhula wina, alankhule ngati manenedwe a Mulungu; wina akatumikira, achite ngati mu mphamvu imene Mulungu ampatsa, kuti m'zonse Mulungu alemekezedwe mwa Yesu Khristu, amene ali nao ulemerero ndi mphamvu kunthawi za nthawi. Amen.
Explore 1 PETRO 4:11
4
1 PETRO 4:16
koma akamva zowawa ngati mkhristu asachite manyazi; koma alemekeze Mulungu m'dzina ili.
Explore 1 PETRO 4:16
5
1 PETRO 4:7
Koma chitsiriziro cha zinthu zonse chili pafupi; chifukwa chake khalani anzeru, ndipo dikirani m'mapemphero
Explore 1 PETRO 4:7
6
1 PETRO 4:12-13
Okondedwa, musazizwe ndi mayesedwe amoto adakugwerani inu akhale chakukuyesani, ngati chinthu chachilendo chachitika nanu: koma popeza mulawana ndi Khristu zowawa zake, kondwerani: kutinso pa vumbulutso la ulemerero wake mukakondwere kwakukulukulu.
Explore 1 PETRO 4:12-13
7
1 PETRO 4:9
mucherezane wina ndi mnzake, osadandaula
Explore 1 PETRO 4:9
8
1 PETRO 4:19
Koteronso iwo akumva zowawa monga mwa chifuniro cha Mulungu aike moyo wao ndi kuchita zokoma m'manja a Wolenga wokhulupirika.
Explore 1 PETRO 4:19
9
1 PETRO 4:1-2
Popeza Khristu adamva zowawa m'thupi, mudzikonzere mtima womwewo; pakuti iye amene adamva zowawa m'thupi walekana nalo tchimo; kuti nthawi yotsalira simukakhalenso ndi moyo m'thupi kutsata zilakolako za anthu, koma chifuniro cha Mulungu.
Explore 1 PETRO 4:1-2
10
1 PETRO 4:14
Mukatonzedwa pa dzina la Khristu, odala inu; pakuti Mzimu wa ulemerero, ndi Mzimu wa Mulungu apuma pa inu.
Explore 1 PETRO 4:14
Home
Bible
Plans
Videos