1
1 MAFUMU 22:22
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Nati, Ndidzatuluka, ndidzakhala mzimu wonama m'kamwa mwa aneneri ake onse. Nati, Udzamnyengadi, nudzakhozanso; tuluka, ukatero kumene.
Compare
Explore 1 MAFUMU 22:22
2
1 MAFUMU 22:23
Ndipo tsopano taonani, Yehova waika mzimu wonama m'kamwa mwa aneneri anu onse awa, ndipo Yehova ananena choipa cha inu.
Explore 1 MAFUMU 22:23
3
1 MAFUMU 22:21
Pamenepo mzimu wina unatuluka, nuima pamaso pa Yehova, nuti, Ndidzamnyenga ndine. Nati Yehova kwa iye, Motani?
Explore 1 MAFUMU 22:21
4
1 MAFUMU 22:20
Nati Yehova, Adzanyenga Ahabu ndani, kuti akwere nagwe ku Ramoti Giliyadi? Ndipo anati wina mwakuti, wina mwakuti.
Explore 1 MAFUMU 22:20
5
1 MAFUMU 22:7
Koma Yehosafati anati, Kodi pano palibe mneneri wina wa Yehova, kuti tifunsire kwa iye?
Explore 1 MAFUMU 22:7
Home
Bible
Plans
Videos