1 MAFUMU 22:23
1 MAFUMU 22:23 BLPB2014
Ndipo tsopano taonani, Yehova waika mzimu wonama m'kamwa mwa aneneri anu onse awa, ndipo Yehova ananena choipa cha inu.