1
1 MAFUMU 16:31
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
Ndipo kunali monga ngati kunamchepera kuyenda m'machimo a Yerobowamu mwana wa Nebati, iye anakwatira Yezebele mwana wamkazi wa Etibaala mfumu ya Asidoni, natumikira Baala, namgwadira.
Compare
Explore 1 MAFUMU 16:31
2
1 MAFUMU 16:30
Ndipo Ahabu mwana wa Omuri anachimwa pamaso pa Yehova koposa onse adamtsogolerawo.
Explore 1 MAFUMU 16:30
Home
Bible
Plans
Videos