1
Masalimo 95:6-7
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
Bwerani, tiyeni tiwerame pomulambira, tiyeni tigwade pamaso pa Yehova Mlengi wathu; pakuti Iye ndiye Mulungu wathu ndipo ife ndife anthu a pabusa pake, ndi nkhosa za mʼdzanja lake.
Compare
Explore Masalimo 95:6-7
2
Masalimo 95:1-2
Bwerani, tiyeni timuyimbire Yehova mwachimwemwe, tiyeni tifuwule kwa Thanthwe la chipulumutso chathu Tiyeni tibwere pamaso pake ndi chiyamiko ndipo mupembedzeni Iyeyo ndi zida zoyimbira ndi nyimbo.
Explore Masalimo 95:1-2
3
Masalimo 95:3
Pakuti Yehova ndi Mulungu wamkulu, mfumu yayikulu pamwamba pa milungu yonse.
Explore Masalimo 95:3
4
Masalimo 95:4
Mʼmanja mwake muli maziko ozama a dziko lapansi, ndipo msonga za mapiri ndi zake.
Explore Masalimo 95:4
Home
Bible
Plans
Videos