1
Masalimo 96:4
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
Pakuti wamkulu ndi Yehova ndipo ndi woyenera kwambiri kumutamanda; ayenera kuopedwa kupambana milungu yonse.
Compare
Explore Masalimo 96:4
2
Masalimo 96:2
Imbirani Yehova, tamandani dzina lake; lalikirani chipulumutso chake tsiku ndi tsiku.
Explore Masalimo 96:2
3
Masalimo 96:1
Imbirani Yehova nyimbo yatsopano; Imbirani Yehova dziko lonse lapansi.
Explore Masalimo 96:1
4
Masalimo 96:3
Lengezani ulemerero wake pakati pa mayiko, ntchito zake zodabwitsa pakati pa mitundu yonse ya anthu.
Explore Masalimo 96:3
5
Masalimo 96:9
Lambirani Yehova mu ulemerero wa chiyero chake; njenjemerani pamaso pake, dziko lonse lapansi.
Explore Masalimo 96:9
Home
Bible
Plans
Videos