1
Masalimo 94:19
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
Pamene nkhawa inakula mʼkati mwanga, chitonthozo chanu chinabweretsa chimwemwe mʼmoyo mwanga.
Compare
Explore Masalimo 94:19
2
Masalimo 94:18
Ndikanena kuti, “Phazi langa likuterereka,” chikondi chanu, Inu Yehova, chimandichirikiza.
Explore Masalimo 94:18
3
Masalimo 94:22
Koma Yehova wakhala linga langa, ndipo Mulungu ndiye thanthwe limene ndimathawirako.
Explore Masalimo 94:22
4
Masalimo 94:12
Wodala munthu amene Inu Yehova mumamulangiza, munthu amene mumamuphunzitsa kuchokera mulamulo lanu
Explore Masalimo 94:12
5
Masalimo 94:17
Yehova akanapanda kundithandiza, bwenzi nditakakhala msanga ku malo achete a imfa.
Explore Masalimo 94:17
6
Masalimo 94:14
Pakuti Yehova sadzawakana anthu ake; Iye sadzasiya cholowa chake.
Explore Masalimo 94:14
Home
Bible
Plans
Videos