1
Masalimo 91:2
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
Ndidzanena za Yehova, “Iye ndiye pothawira panga ndi linga langa, Mulungu wanga amene ndimadalira.”
Compare
Explore Masalimo 91:2
2
Masalimo 91:1
Iye amene amakhala mu mthunzi wa Wammwambamwamba adzapuma mu mthunzi wa Wamphamvuzonse.
Explore Masalimo 91:1
3
Masalimo 91:15
Adzandiyitana, ndipo ndidzamuyankha; ndidzakhala naye pa mavuto, ndidzamupulumutsa ndi kumulemekeza.
Explore Masalimo 91:15
4
Masalimo 91:11
Pakuti adzalamulira angelo ake za iwe, kuti akutchinjirize mosamala pa njira zako zonse
Explore Masalimo 91:11
5
Masalimo 91:4
Adzakuphimba ndi nthenga zake, ndipo udzapeza malo othawira mʼmapikomo; kukhulupirika kwake kudzakhala chishango chako ndi lihawo.
Explore Masalimo 91:4
6
Masalimo 91:9-10
Pakuti wasankha Wammwambamwamba kukhala malo ako okhalamo; wavomera Yehova kukhala kothawira kwako. Choncho palibe choyipa chimene chidzakugwera, zoopsa sizidzafika pafupi ndi tenti yako.
Explore Masalimo 91:9-10
7
Masalimo 91:3
Ndithu, Iye adzakupulumutsa ku msampha wa mlenje ndi ku mliri woopsa
Explore Masalimo 91:3
8
Masalimo 91:7
Anthu 1,000 atha kufa pambali pako, anthu 10,000 kudzanja lako lamanja, koma zoopsazo sizidzafika pafupi ndi iwe.
Explore Masalimo 91:7
9
Masalimo 91:5-6
Sudzachita mantha ndi zoopsa za usiku, kapena muvi wowuluka masana, kapena mliri umene umayenda mu mdima, kapena zowononga za pa nthawi ya masana.
Explore Masalimo 91:5-6
Home
Bible
Plans
Videos