1
Masalimo 92:12-13
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
Anthu olungama adzaphuka ngati mtengo wa mgwalangwa, adzakula ngati mkungudza wa ku Lebanoni; odzalidwa mʼnyumba ya Yehova, adzakula bwino mʼmabwalo a Mulungu wathu.
Compare
Explore Masalimo 92:12-13
2
Masalimo 92:14-15
Iwo adzaberekabe zipatso mu ukalamba wawo, adzakhala anthete ndi obiriwira, kulengeza kuti, “Yehova ndi wolungama; Iye ndiye Thanthwe langa, ndipo mwa Iye mulibe choyipa.”
Explore Masalimo 92:14-15
Home
Bible
Plans
Videos