1
Masalimo 90:12
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
Tiphunzitseni kuwerenga masiku athu molondola, kuti tikhale ndi mtima wanzeru.
Compare
Explore Masalimo 90:12
2
Masalimo 90:17
Kukoma mtima kwa Ambuye Mulungu wathu kukhale pa ife; tikhazikitsireni ntchito ya manja athu; inde, khazikitsani ntchito ya manja athu.
Explore Masalimo 90:17
3
Masalimo 90:14
Mutikhutitse mmawa ndi chikondi chanu chosatha, kuti tiyimbe ndi chimwemwe ndi kukhala okondwa masiku athu onse.
Explore Masalimo 90:14
4
Masalimo 90:2
Mapiri asanabadwe, musanalenge nʼkomwe dziko lapansi ndi dziko lonse, kuyambira muyaya mpaka muyaya Inu ndinu Mulungu.
Explore Masalimo 90:2
5
Masalimo 90:1
Ambuye, mwakhala muli malo athu okhalamo pa mibado yonse.
Explore Masalimo 90:1
6
Masalimo 90:4
Pakuti zaka 1,000 pamaso panu zili ngati tsiku limene lapita kapena ngati kamphindi ka usiku.
Explore Masalimo 90:4
Home
Bible
Plans
Videos