1
Machitidwe a Atumwi 3:19
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
Chifukwa chake, lapani, bwererani kwa Mulungu, kuti machimo anu afafanizidwe, kuti nthawi ya kutsitsimuka ibwere kuchokera kwa Ambuye
Compare
Explore Machitidwe a Atumwi 3:19
2
Machitidwe a Atumwi 3:6
Petro anati kwa iye, “Ine ndilibe siliva kapena golide, koma chimene ndili nacho ndikupatsa. Mʼdzina la Yesu Khristu wa ku Nazareti, yenda.”
Explore Machitidwe a Atumwi 3:6
3
Machitidwe a Atumwi 3:7-8
Ndipo anamugwira dzanja lamanja, namuthandiza kuti ayimirire ndipo nthawi yomweyo mapazi ake ndi akakolo ake analimba. Iye analumpha ndi kuyamba kuyenda. Kenaka analowa nawo pamodzi mʼbwalo la Nyumba ya Mulungu, akuyenda ndi kulumpha ndiponso kuyamika Mulungu.
Explore Machitidwe a Atumwi 3:7-8
4
Machitidwe a Atumwi 3:16
Mwachikhulupiriro mʼdzina la Yesu, munthu uyu amene mukumuona ndi kumudziwa analimbikitsidwa. Mʼdzina la Yesu ndi chikhulupiriro chimene chili mwa iye chamuchiritsa kwathunthu, monga nonse mukuona.
Explore Machitidwe a Atumwi 3:16
Home
Bible
Plans
Videos