1
Machitidwe a Atumwi 4:12
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
Chipulumutso sichipezeka mwa wina aliyense; pakuti palibe dzina lina pansi pa thambo limene lapatsidwa kwa anthu limene tiyenera kupulumutsidwa nalo.”
Compare
Explore Machitidwe a Atumwi 4:12
2
Machitidwe a Atumwi 4:31
Iwo atatha kupemphera, malo amene anasonkhanapo anagwedezeka. Ndipo iwo onse anadzazidwa ndi Mzimu Woyera ndipo anayankhula Mawu a Mulungu molimba mtima.
Explore Machitidwe a Atumwi 4:31
3
Machitidwe a Atumwi 4:29
Tsopano, Ambuye taonani kuti atiopseza, tithandizeni ife atumiki anu, kuti tiyankhule mawu anu molimba mtima.
Explore Machitidwe a Atumwi 4:29
4
Machitidwe a Atumwi 4:11
Iye ndi “ ‘Mwala umene amisiri omanga nyumba anawukana, umenewo wasanduka mwala wa pa ngodya!’
Explore Machitidwe a Atumwi 4:11
5
Machitidwe a Atumwi 4:13
Ataona kulimba mtima kwa Petro ndi Yohane ndi kuzindikira kuti anali osaphunzira, anthu wamba, anadabwa kwambiri ndipo anazindikira kuti anthuwa anakhala pamodzi ndi Yesu.
Explore Machitidwe a Atumwi 4:13
6
Machitidwe a Atumwi 4:32
Okhulupirira onse anali a mtima umodzi, ndi maganizo amodzi. Palibe munthu amene amati zomwe anali nazo zinali zake zokha, koma amagawana chilichonse chimene anali nacho.
Explore Machitidwe a Atumwi 4:32
Home
Bible
Plans
Videos