Machitidwe a Atumwi 3:6
Machitidwe a Atumwi 3:6 CCL
Petro anati kwa iye, “Ine ndilibe siliva kapena golide, koma chimene ndili nacho ndikupatsa. Mʼdzina la Yesu Khristu wa ku Nazareti, yenda.”