1
ZEKARIYA 6:12
Buku Lopatulika
nunene naye, kuti, Atero Yehova wa makamu, ndi kuti, Taonani, munthu dzina lake ndilo Mphukira, ndipo adzaphuka m'malo mwake, nadzamanga Kachisi wa Yehova
Compare
Explore ZEKARIYA 6:12
2
ZEKARIYA 6:13
inde adzamanga Kachisi wa Yehova; nadzasenza ulemererowo, nadzakhala ndi kulamulira pa mpando wachifumu wake; nadzakhala wansembe pampando wachifumu wake; ndi uphungu wa mtendere udzakhala pakati pa iwo awiri.
Explore ZEKARIYA 6:13
Home
Bible
Plans
Videos