1
YOHANE 4:24
Buku Lopatulika
Mulungu ndiye mzimu; ndipo omlambira Iye ayenera kumlambira mumzimu ndi m'choonadi.
Qhathanisa
Hlola YOHANE 4:24
2
YOHANE 4:23
Koma ikudza nthawi, ndipo tsopano ilipo, imene olambira oona adzalambira Atate mumzimu ndi m'choonadi; pakuti Atate afuna otere akhale olambira ake.
Hlola YOHANE 4:23
3
YOHANE 4:14
koma iye wakumwa madzi amene Ine ndidzampatsa sadzamva ludzu nthawi zonse; koma madzi amene Ine ndidzampatsa adzakhala mwa iye kasupe wa madzi otumphukira kumoyo wosatha.
Hlola YOHANE 4:14
4
YOHANE 4:10
Yesu anayankha nati kwa iye, Ukadadziwa mtulo wa Mulungu, ndi Iye amene alinkunena ndi iwe, Undipatse Ine ndimwe; ukadapempha Iye, ndipo akadakupatsa madzi amoyo.
Hlola YOHANE 4:10
5
YOHANE 4:34
Yesu ananena nao, Chakudya changa ndicho kuti ndichite chifuniro cha Iye amene anandituma Ine, ndi kutsiriza ntchito yake.
Hlola YOHANE 4:34
6
YOHANE 4:11
Mkaziyo ananena ndi Iye, Ambuye, mulibe chotungira madzi, ndi chitsime chili chakuya; ndipo mwatenga kuti madzi amoyo?
Hlola YOHANE 4:11
7
YOHANE 4:25-26
Mkazi ananena ndi Iye, Ndidziwa kuti Mesiya adza (wotchedwa Khristu): akadzadza Iyeyu, adzatiuza zonse. Yesu ananena naye, Ine wakulankhula nawe ndine amene.
Hlola YOHANE 4:25-26
8
YOHANE 4:29
Tiyeni, mukaone munthu, amene anandiuza zinthu zilizonse ndinazichita: ameneyu sali Khristu nanga?
Hlola YOHANE 4:29
Ikhaya
IBhayibheli
Amapulani
Amavidiyo