1
LUKA 21:36
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Koma inu dikirani nyengo zonse, ndi kupemphera, kuti mukalimbike kupulumuka zonse zimene zidzachitika, ndi kuimirira pamaso pa Mwana wa Munthu.
Ṣe Àfiwé
Ṣàwárí LUKA 21:36
2
LUKA 21:34
Koma mudziyang'anire nokha, kuti kapena mitima yanu ingalemetsedwe ndi madyaidya ndi kuledzera, ndi zosamalira za moyo uno, ndi kuti tsiku ilo lingafikire inu modzidzimutsa ngati msampha
Ṣàwárí LUKA 21:34
3
LUKA 21:19
Mudzakhala nao moyo wanu m'chipiriro.
Ṣàwárí LUKA 21:19
4
LUKA 21:15
Pakuti Ine ndidzakupatsani inu kamwa ndi nzeru, zimene adani anu onse sadzatha kuzikana kapena kuzitsutsa.
Ṣàwárí LUKA 21:15
5
LUKA 21:33
Kumwamba ndi dziko lapansi zidzapita; koma mau anga sadzapita.
Ṣàwárí LUKA 21:33
6
LUKA 21:25-27
Ndipo kudzakhala zizindikiro pa dzuwa ndi mwezi ndi nyenyezi; ndi pa dziko lapansi chisauko cha mitundu ya anthu, alikuthedwa nzeru pa mkukumo wake wa nyanja ndi mafunde ake; anthu akukomoka ndi mantha, ndi kuyembekezera zinthu zilinkudza kudziko lapansi; pakuti mphamvu zakumwamba zidzagwedezeka. Ndipo pamenepo adzaona Mwana wa Munthu alinkudza mu mtambo ndi mphamvu ndi ulemerero waukulu.
Ṣàwárí LUKA 21:25-27
7
LUKA 21:17
Ndipo anthu onse adzadana ndi inu chifukwa cha dzina langa.
Ṣàwárí LUKA 21:17
8
LUKA 21:11
ndipo kudzakhala zivomezi zazikulu, ndi njala ndi miliri m'malo akutiakuti, ndipo kudzakhala zoopsa ndi zizindikiro zazikulu zakumwamba.
Ṣàwárí LUKA 21:11
9
LUKA 21:9-10
Ndipo pamene mudzamva za nkhondo ndi mapanduko, musaopsedwa; pakuti ziyenera izi ziyambe kuchitika; koma mathedwe sakhala pomwepo. Pamenepo ananena nao, Mtundu wa anthu udzaukira pa mtundu wina, ndipo ufumu pa ufumu wina
Ṣàwárí LUKA 21:9-10
10
LUKA 21:25-26
Ndipo kudzakhala zizindikiro pa dzuwa ndi mwezi ndi nyenyezi; ndi pa dziko lapansi chisauko cha mitundu ya anthu, alikuthedwa nzeru pa mkukumo wake wa nyanja ndi mafunde ake; anthu akukomoka ndi mantha, ndi kuyembekezera zinthu zilinkudza kudziko lapansi; pakuti mphamvu zakumwamba zidzagwedezeka.
Ṣàwárí LUKA 21:25-26
11
LUKA 21:10
Pamenepo ananena nao, Mtundu wa anthu udzaukira pa mtundu wina, ndipo ufumu pa ufumu wina
Ṣàwárí LUKA 21:10
12
LUKA 21:8
Ndipo Iye anati, Yang'anirani musasocheretsedwe; pakuti ambiri adzadza m'dzina langa, nadzanena, Ndine amene; ndipo, Nthawi yayandikira; musawatsate pambuyo pao.
Ṣàwárí LUKA 21:8
Ilé
Bíbélì
Àwon ètò
Àwon Fídíò