Ntc. 16:27-28
Ntc. 16:27-28 BLY-DC
Woyang'anira ndende uja atadzuka, naona kuti zitseko zonse za ndende nzotsekuka, adaayesa kuti akaidi athaŵa. Pamenepo adasolola lupanga lake nati adziphe. Koma Paulo adafuula kuti, “Iwe usadzipweteke! Tonse tilipo!”