1
Ntc. 7:59-60
Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa
Pamene anthuwo ankamuponya miyala, Stefano adayamba kupemphera kuti, “Ambuye Yesu, landirani mzimu wanga.” Ndipo adagwada pansi nafuula kwakukulu kuti, “Ambuye, musaŵaŵerengere tchimoli.” Atanena mau ameneŵa, adafa.
Paghambingin
I-explore Ntc. 7:59-60
2
Ntc. 7:49
“Chauta akuti, ‘Kumwamba ndi mpando wanga waufumu, dziko lapansi ndi chopondapo mapazi anga. Kodi mudzandimangira nyumba yotani? Kapena malo opumuliramo Inewo ngotani?
I-explore Ntc. 7:49
3
Ntc. 7:57-58
Koma iwo adafuula kwambiri, natseka m'makutu mwao, namgudukira onse pamodzi. Adamtulutsira kunja kwa mzinda, nakamponya miyala. Mboni zidasungiza zovala zao munthu wachinyamata wina, dzina lake Saulo.
I-explore Ntc. 7:57-58
Home
Biblia
Mga Gabay
Mga Palabas